Ngakhale tikutumiza ma numbers sizikuyenda pano pa owinna.com chonde chonde admin tithandizeni tiuzeni zoona kuti tiyendele zimodzi ngati tidzalandile mphoto zathu.
0995587166
Komano zanyanya 0991769328
iiii admin kodi mukutiva? 0995587166
0888490783
0991769328 komono tilandiladi?
0995587166 apa ndiye sizilibwino
Kod last time munagwilizana zoti buanji and ndalama ziperekedwa liti coz munabwera kutiuza kt admin apereka ndalama zambuyo
0991769328
Stella kaunda. UVETSETSE... Tinagwilizana kuti kuyambila pa 24 August aliyese asayikeso ma prediction pokhapokha apereke kaye ndalama zose kuyambila sabata yothera 26 July m'paka sabata yothera 23 August. Ndiye admin analonjeza kuti ndalama apereka. Ndiye tinaperekaso m'pata kuti amene angafune atha kumayika ma predictions. M'pake mukuwona kuti wena akuyika wena anayima kaye kudikila ndalama. Wilfred Given ndiwe mwa m'modzi amene sukumavela malamulo apano pa owinna.com tikati tisayike ma predictions iwe ukumakhala oyamba kuyika ma prediction. USAMALE.
Ineo ndikuona kuti buanji tidikile kae mpaka ndalama zonse zomwe yapanga mbuyo mu zitalowa kwa anthu oenela chifukwa apapa kuli zii even admin sakuyankha and sakupereka chilimbikiso chirichonse so I suggest tiime kae
Tayamba kupereka mphoto zanu. Amene anawina Sabata yothera 26 July alandira mphoto zawo. Ena azilandira masiku akubwera wa.
Moni nose pano pa owinna.com photo za sabata yothera 26 July admin akuti apereka ndiposo ena mwamene anachita mwayi sabata imeneyi atitsimikizila kuti alandiladi. Ndiye tikupeleso ufulu kwamene tingafune tickets ma predictions. NB: UTHENGA KWA ADMIN WATHU MPHOTOZIKUFUNIKA ZOSE POFIKA MONDAY PA 7 SEPTEMBER 2026. KUPANDA APO TIDZAWONETSELA KUKWIYA KWATHU CHIFUKWA ALIYESE ANACHITA MWAYI MPHOTO ZAWO AKUZIFUNA.
0897788997
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores