Ngakhale tikutumiza ma numbers sizikuyenda pano pa owinna.com chonde chonde admin tithandizeni tiuzeni zoona kuti tiyendele zimodzi ngati tidzalandile mphoto zathu.
Ineo ndikuona kuti buanji tidikile kae mpaka ndalama zonse zomwe yapanga mbuyo mu zitalowa kwa anthu oenela chifukwa apapa kuli zii even admin sakuyankha and sakupereka chilimbikiso chirichonse so I suggest tiime kae
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores