Ngakhale tikutumiza ma numbers sizikuyenda pano pa owinna.com chonde chonde admin tithandizeni tiuzeni zoona kuti tiyendele zimodzi ngati tidzalandile mphoto zathu.
Moni nose pano pa owinna.com photo za sabata yothera 26 July admin akuti apereka ndiposo ena mwamene anachita mwayi sabata imeneyi atitsimikizila kuti alandiladi. Ndiye tikupeleso ufulu kwamene tingafune tickets ma predictions. NB: UTHENGA KWA ADMIN WATHU MPHOTOZIKUFUNIKA ZOSE POFIKA MONDAY PA 7 SEPTEMBER 2026. KUPANDA APO TIDZAWONETSELA KUKWIYA KWATHU CHIFUKWA ALIYESE ANACHITA MWAYI MPHOTO ZAWO AKUZIFUNA.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores