Timu ya Kukoma Ntopwa Queens yafika m'dziko la South Africa komwe akukasewera mu mpikisano wa COSAFA CAF Women's Championship.
Timuyi ikumana ndi Mamelodi Sundowns mawa mu masewero awo oyamba ku mpikisanowu.
Aka ndi kachiwiri kuti timuyi isewere mu mpikisanowu poti mu chaka cha 2023 inapitanso mdzikolo.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores