Timu ya Kukoma Ntopwa Queens tsopano ikuyembekezeka kunyamuka kulowera m'dziko la South Africa komwe akatenge nawo mbali mu mpikisano wa COSAFA CAF Women's Championship.
Timuyi inali ndi malingaliro oti asapitenso kutsatira kuti amasowa ndalama yakunja yomwe imafunikira kuti ayendere kupita mdzikolo komatu tsopano yapezeka ndipo malingana ndi nyuzipepala ya Nation, timuyi yanyamuka tsopano.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores