Timu ya Jenda United yomwe imasewera mu ligi ya NBS NATIONAL DIVISION LEAGUE yaimitsa ntchito mphunzitsi wamkulu wa timuyi a Obvious Banda.
Malingana ndi timuyi yati yachita izi kusatira kusachita bwino Kwa timuyi pomwe yagonja masewero atatu omwe yasewera.
Ndipo timuyi yati tsogolo la mphunzitsi lidziwika bwino akulu akulu a timuyi akakumana.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores