Timu ya Nyasa Big Bullets yati ndiyokhutira ndi momwe Energem International Bonanza yomwe inachititsa mu mzinda wa Blantyre yayendera.
Mmodzi wa akuluakulu a Bullets, Kelvin Moyo, wanena izi.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores