Ngakhale tikutumiza ma numbers sizikuyenda pano pa owinna.com chonde chonde admin tithandizeni tiuzeni zoona kuti tiyendele zimodzi ngati tidzalandile mphoto zathu.
Tikuyesetsa kuti nonse mulandire mphoto zanu nthawi imodzi, koma zikuchedwerapo. Pepani mwina sitikwanitsa kufika pa 7 September, koma tipitiriza kumapereka mphoto mmene zikupezekera. Zikomo.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores