Osagie wachoka ku Silver
Timu ya Silver Strikers yalengeza zoti katswiri wawo wosewera kutsogolo ku timuyi, Friday Osagie, tsopano wachoka atangokhalako miyezi isanu ndi imodzi okha.
Timuyi yalengeza za kuchoka kwa katswiriyu lachitatu masana kudzera pa tsamba lawo la mchezo.
Osagie, yemwe kwao ndi ku Nigeria, anapita kutimuyi pansi pa Peter Mponda ndipo wathandizira kutenga chikho cha TNM chaka chatha.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores