Timu ya Mighty Wanderers yalengeza kuti yatenga katswiri wosewera pakati kutimu ya Ekhaya FC, Rajab Nyirenda kuti alowe mmalo mwa Francisco Madinga.
Iye wasaina mgwirizano wa zaka ziwiri ndi timuyi.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores