Katswiri woimba nyimbo za uzimu mdziko muno Dr Namadingo wauza otchinga pagolo wa Flames Charles Thom kuti asankhe chinthu chomwe akufuna amugulire kuchokera ku South Africa.
Dr Namadingo ati iyi ndi njira imodzi yomuthokoza goloboyi wa Flames pa momwe anasewelera kumpikisano wa AFCON.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores