Timu ya Burkina Faso yafika mdziko muno patsogolo pa masewero ake mawa ndi Flames.
Timuyi inagonjetsa Flames Lachinayi lapitali 3-1.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores