Timu ya Blue Eagles yati m'masewero omwe ali nawo m'chigawo cha kumpoto apeza wosewera ena oti atumikire timuyi mu 2020.
Wapampando wa Blue Eagles, Alexander Ngwala, ndiye wanena izi.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores