Anthu okonda masewero mu mzinda wa Blantyre ati bungwe la FAM lisachite machawi polemba mphunzitsi wina watsopano.
Anthu-wa ati amupase nthawi Meke Mwase ponena kuti waonetsa kuthekera kwake.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores