Mabungwe oyendetsa za masewero adandaula za mtengo woyezetsera osewera matenda a COVID-19. Kuyezetsaku ndi imodzi mwanjira zoti matimu akuyenera kutsatira kuti mpira uyambenso ku Malawi. Nation Online www.mwnation.com
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores