🚨 Nico Williams signs a new deal
Athletic Club forward Nico Williams has signed a new contract at the club until 2035. 🗣️ 'The most important thing is to listen to your heart' 🗣️ 'I'm where I want to be, with my people, this is my home. Aupa Athletic!
MUKUWONJEZA NAZOTU MAGAME MUKUMAYIKA NTHAWI YANUYANU YOTI YATSALA PANG'ONO KUYAMBA NDIYE BWANJI NGATI ZUMAVUTA KUYIKA MUDZINGOLEKA.
ZOONA MAGAME MUNZIIKA LELO OTI ASWWELA MAWA OSATI ZACHAMBAZI.
ZACHIBWANA MUKUMAPANGAZI MAGAME MUDZIIKILA PATALI TILI NDI ZINA ZOCHITATU NDALAMA YANUYISO NDIYOCHEPA.
PAFUNIKA ZITHE ZIMENEZI MUDZIIKILA PATALI MAGAME OSATI IZIZI.
KODINO MUMAGANIZA BWANJIDI NGATI TULIMBILANA NDALAMALAMASO KUTI MUDZIIKA MAGAME MOCHEDWA DELE?.
AAAA ZACHAMBA IZI.
MAGAME ALERO MUDZIIKA DZULO OSATI ZACHIBWANAZI.
ISHIII KOMA AMUMBA ZUMATIWAWATU IFE
MASANJE WENIWENI MUGANIZE BWINO.
ANTHU TIKUDANDAULA MAKA PAMAYIKIDWE AMAGAME PA OWINNA.COM MUKUMAYIKA MOCHEDWA KOMASO TSIKO LOMWELO NTHAWISO YOTHA KALE PAMENE WENA AMAKHALA KUTI ATULUKA CHIFUKWA CHA IZI AMENE ANALI PAMBUYO AKAWONA MWACHANGU ZIMAWAPANGITSA KUKOKELA NAMBALA ZOMWE ZILI NGATI CHINYENGO. NDIYE PAKUFUNIKA MUDZIIKA PAKAMODZI ZA WEEK YONSE OSATI MUKUMAPANGAZI.
Pempho lanu lamveka ndithu. Tidziyesetsa kuikiratu magemu tsiku losewera lisanafike kuti tidzikupatsani nthawi yolosera yokwanira.
Tinachedwa kuona magemu a COSAFA Under 20 koma tinaona kuti nkofunika kwambiri kuti anthu atsatire mmene gemu ya Malawi ndi Zimbabwe iyendere. Nchifukwa chake tinaiika lero lomwe.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores