Timu ya Ekhaya FC yatsimikiza kuti yalekana ndi katswiri womwetsa zigoli, Mwai Banda, yemwe wathetsa mgwirizano wake ndi timuyi.
Martial anali m'modzi mwa osewera omwe anathandiza timuyi kuti ilowe mu ligi ya TNM Koma kuti nthawi yake yosewera inali yochepa.
Timuyi yamufunira zabwino katswiriyu pomwe akuyamba umoyo wina.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores