Mlembi wa komiti yoyendetsa masewero ku Mchinji, Thom Lemison, walangiza matimu kuti atsatire ndondomeko zomwe azaumoyo akhazikitsa pofuna kupewa matenda a Covid-19.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores