Osewera wa Nyasa Big Bullets, Azizi Mwakifuna akusewera timu ya Mbeya mdziko la Tanzania.
Mwakifuna akusewelera timuyi opanda zikalata zomulola kutero kuchokera ku timu yake ya Bullets.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores